Ekisodo 40:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Mose anachita zonse monga mmene Yehova anamulamulira.+ Anachitadi momwemo. Deuteronomo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.
5 Taonani, ndakuphunzitsani malangizo+ ndi zigamulo,+ monga mmene Yehova Mulungu wanga wandilamulira, kuti muzikatsatira zimenezo pamene mukukhala m’dziko limene mukupita kukalitenga kukhala lanu.