Numeri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti azitulutsa mumsasa munthu aliyense wakhate,+ aliyense wakukha kumaliseche,+ ndi aliyense wodetsedwa chifukwa chokhudza mtembo wa munthu.+ Numeri 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aliyense wokhudza mtembo wa munthu aliyense,+ nayenso azikhala wodetsedwa masiku 7.+
2 “Lamula ana a Isiraeli kuti azitulutsa mumsasa munthu aliyense wakhate,+ aliyense wakukha kumaliseche,+ ndi aliyense wodetsedwa chifukwa chokhudza mtembo wa munthu.+