Deuteronomo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa nthawi imeneyo tinalanda mizinda yake yonse. Panalibe mzinda umene sitinawalande. Tinalanda mizinda 60+ m’chigawo chonse cha Arigobi,+ m’dera lonse la ufumu wa Ogi ku Basana.+ Salimo 135:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+
4 Pa nthawi imeneyo tinalanda mizinda yake yonse. Panalibe mzinda umene sitinawalande. Tinalanda mizinda 60+ m’chigawo chonse cha Arigobi,+ m’dera lonse la ufumu wa Ogi ku Basana.+
11 Anaphanso Sihoni mfumu ya Aamori+Ndi Ogi mfumu ya Basana,+Ndipo anafafaniza maufumu onse a ku Kanani.+