Numeri 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anayamba kukhala kumeneko chifukwa Hesiboni unali mzinda wa Sihoni.+ Sihoni inali mfumu ya Aamori,+ ndipo iye ndiye anamenyana ndi mfumu ya Mowabu m’mbuyomo, n’kulanda dziko lonse limene linali m’manja mwake mpaka kuchigwa cha Arinoni.+ Yoswa 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+
26 Anayamba kukhala kumeneko chifukwa Hesiboni unali mzinda wa Sihoni.+ Sihoni inali mfumu ya Aamori,+ ndipo iye ndiye anamenyana ndi mfumu ya Mowabu m’mbuyomo, n’kulanda dziko lonse limene linali m’manja mwake mpaka kuchigwa cha Arinoni.+
17 Hesiboni,+ ndi midzi yake yonse+ imene inali m’malo okwererapowo. Linaphatikizaponso Diboni,+ Bamoti-baala,+ Beti-baala-meoni,+