Numeri 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 kuyambira azaka 30 mpaka 50, onse olowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako,+ Numeri 4:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 amene anawerengedwa malinga ndi mabanja awo, onse pamodzi anakwana 3,200.+