Numeri 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako. Numeri 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uwerenge kuyambira azaka 30 mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako. Numeri 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Uwerenge kuyambira azaka 30 mpaka 50, onse olowa m’gulu la ogwira ntchito pachihema chokumanako.+ Numeri 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anawerenga kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse amene analowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako.+ Numeri 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 kuyambira azaka 30 mpaka 50, onse amene analowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako,+ Numeri 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye azingothandizira abale ake m’chihema chokumanako pochita utumiki wawo, koma asatumikire. Umu ndi mmene uzichitira ndi Alevi malinga ndi ntchito zawo.”+
3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako.
35 Anawerenga kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse amene analowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako.+
26 Iye azingothandizira abale ake m’chihema chokumanako pochita utumiki wawo, koma asatumikire. Umu ndi mmene uzichitira ndi Alevi malinga ndi ntchito zawo.”+