Numeri 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako. Numeri 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye azingothandizira abale ake m’chihema chokumanako pochita utumiki wawo, koma asatumikire. Umu ndi mmene uzichitira ndi Alevi malinga ndi ntchito zawo.”+
3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako.
26 Iye azingothandizira abale ake m’chihema chokumanako pochita utumiki wawo, koma asatumikire. Umu ndi mmene uzichitira ndi Alevi malinga ndi ntchito zawo.”+