Numeri 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye azingothandizira abale ake amene akugwira ntchito pachihema chokumanako, koma asamatumikire kuchihemako. Izi ndi zimene uzichita ndi Alevi mogwirizana ndi ntchito zawo.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:26 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 25
26 Iye azingothandizira abale ake amene akugwira ntchito pachihema chokumanako, koma asamatumikire kuchihemako. Izi ndi zimene uzichita ndi Alevi mogwirizana ndi ntchito zawo.”+