Numeri 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye azingothandizira abale ake m’chihema chokumanako pochita utumiki wawo, koma asatumikire. Umu ndi mmene uzichitira ndi Alevi malinga ndi ntchito zawo.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:26 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 25
26 Iye azingothandizira abale ake m’chihema chokumanako pochita utumiki wawo, koma asatumikire. Umu ndi mmene uzichitira ndi Alevi malinga ndi ntchito zawo.”+