Ekisodo 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wonse wa pachihema chopatulika, zikhomo zonse za chihema, ndi zikhomo za bwalo zikhale zamkuwa.+
19 Ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wonse wa pachihema chopatulika, zikhomo zonse za chihema, ndi zikhomo za bwalo zikhale zamkuwa.+