Ekisodo 38:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zikhomo zonse za chihema chopatulika ndi za bwalo lonse zinali zamkuwa.+ Numeri 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ntchito imene ana a Merari anapatsidwa inali yosamalira mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ zitsulo zokhazikapo mafelemu ndi mizati, ziwiya zonse+ ndi zina zonse zokhudza utumiki umenewu.+
36 Ntchito imene ana a Merari anapatsidwa inali yosamalira mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ zitsulo zokhazikapo mafelemu ndi mizati, ziwiya zonse+ ndi zina zonse zokhudza utumiki umenewu.+