Yoswa 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Dziko lanu lidzayambira kuchipululu ndi ku Lebanoni uyu mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate, dziko lonse la Ahiti+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu, kolowera dzuwa.+ Yoswa 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malire a kumadzulo anali Nyanja Yaikulu+ ndi gombe lake. Amenewa ndiwo anali malire onse a ana a Yuda potsata mabanja awo.
4 Dziko lanu lidzayambira kuchipululu ndi ku Lebanoni uyu mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate, dziko lonse la Ahiti+ mpaka kukafika ku Nyanja Yaikulu, kolowera dzuwa.+
12 Malire a kumadzulo anali Nyanja Yaikulu+ ndi gombe lake. Amenewa ndiwo anali malire onse a ana a Yuda potsata mabanja awo.