Numeri 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwa ana a Gerisoni, panali banja la Alibini+ ndi banja la Asimeyi.+ Awa ndiwo anali mabanja a Agerisoni. Numeri 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mabanja a Agerisoni anali kukhala kumbuyo kwa chihema chopatulika.+ Anali kumanga msasa wawo kumadzulo.
21 Mwa ana a Gerisoni, panali banja la Alibini+ ndi banja la Asimeyi.+ Awa ndiwo anali mabanja a Agerisoni.
23 Mabanja a Agerisoni anali kukhala kumbuyo kwa chihema chopatulika.+ Anali kumanga msasa wawo kumadzulo.