Numeri 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+ Numeri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Uike Aroni ndi ana ake kukhala ansembe, kuti azigwira ntchito yaunsembe.+ Aliyense amene si Mlevi akayandikira malowo, aziphedwa.”+
3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+
10 Uike Aroni ndi ana ake kukhala ansembe, kuti azigwira ntchito yaunsembe.+ Aliyense amene si Mlevi akayandikira malowo, aziphedwa.”+