Numeri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Azisamalira ziwiya zonse+ za pachihema chokumanako, monga gawo limodzi la ntchito za ana a Isiraeli zimene a fuko la Leviwo aziwagwirira potumikira pachihema chopatulika.+
8 Azisamalira ziwiya zonse+ za pachihema chokumanako, monga gawo limodzi la ntchito za ana a Isiraeli zimene a fuko la Leviwo aziwagwirira potumikira pachihema chopatulika.+