Numeri 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli.
14 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli.