Numeri 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuchokera ku fuko la Gadi,+ Eliyasafu+ mwana wa Deyueli,+ Numeri 7:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pa tsiku la 6 panali mtsogoleri wa ana a Gadi, Eliyasafu+ mwana wa Deyueli. Numeri 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Gadi anali Eliyasafu,+ mwana wa Deyueli.