Numeri 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli. Numeri 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Gadi anali Eliyasafu,+ mwana wa Deyueli.
14 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli.