Numeri 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Gadi anali Eliyasafu,+ mwana wa Deyueli.