-
Oweruza 16:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Zitatero, Delila anagonetsa Samisoni tulo pamawondo ake, ndipo anaitana mwamuna wina amene anam’meta zingongo 7 za m’mutu mwake. Kenako Delila anayamba kukula mphamvu pa Samisoni ndipo mphamvu za Samisoni zinam’chokera.
-