Levitiko 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo. Levitiko 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Tsopano lamulo la nsembe yambewu+ lili motere: Ana a Aroni azibweretsa nsembeyi pamaso pa Yehova patsogolo pa guwa lansembe.
2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.
14 “‘Tsopano lamulo la nsembe yambewu+ lili motere: Ana a Aroni azibweretsa nsembeyi pamaso pa Yehova patsogolo pa guwa lansembe.