Ekisodo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mkate wopanda chofufumitsa, mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta ndi timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta.+ Uzipange ndi ufa wa tirigu wosalala. Numeri 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera.+ Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+
2 mkate wopanda chofufumitsa, mkate wozungulira woboola pakati, wopanda chofufumitsa, wothira mafuta ndi timitanda ta mkate topyapyala topanda chofufumitsa, topaka mafuta.+ Uzipange ndi ufa wa tirigu wosalala.
13 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera.+ Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+