Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.

  • Numeri 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.

  • Numeri 7:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:61
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:67
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 67 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:73
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 73 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:79
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 79 Iye anapereka mbale yaikulu imodzi yasiliva yolemera masekeli 130, ndiponso mbale yolowa imodzi yasiliva yolemera masekeli 70, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera. Mbale ziwiri zonsezo zinali zodzaza ndi ufa wosalala wothira mafuta, wa nsembe yambewu.+

  • Numeri 7:87
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 87 Nyama zonse zoperekedwa za nsembe yopsereza+ zinalipo ng’ombe 12 zamphongo, nkhosa 12 zamphongo, ndi ana a nkhosa 12 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Zinaperekedwa limodzi ndi nsembe zawo zambewu.+ Atsogoleriwa anaperekanso ana a mbuzi 12 a nsembe yamachimo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena