-
Numeri 7:87Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
87 Nyama zonse za nsembe yopsereza zinalipo ngʼombe 12 zamphongo, nkhosa 12 zamphongo ndi ana a nkhosa 12 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Nyamazi anazipereka limodzi ndi nsembe zake zambewu. Atsogoleriwa anaperekanso mbuzi zingʼonozingʼono 12 za nsembe yamachimo.
-