87 Nyama zonse zoperekedwa za nsembe yopsereza+ zinalipo ng’ombe 12 zamphongo, nkhosa 12 zamphongo, ndi ana a nkhosa 12 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Zinaperekedwa limodzi ndi nsembe zawo zambewu.+ Atsogoleriwa anaperekanso ana a mbuzi 12 a nsembe yamachimo.+