Numeri 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 kuchokera ku fuko la Isakara,+ Netaneli+ mwana wa Zuwara, Numeri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Isakara.+ Mtsogoleri wa ana a Isakara ndi Netaneli,+ mwana wa Zuwara. Numeri 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Isakara anali Netaneli,+ mwana wa Zuwara.
5 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Isakara.+ Mtsogoleri wa ana a Isakara ndi Netaneli,+ mwana wa Zuwara.