Numeri 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 kuchokera ku fuko la Isakara,+ Netaneli+ mwana wa Zuwara, Numeri 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Netaneli+ mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa fuko la Isakara, anapereka zopereka zake pa tsiku lachiwiri. Numeri 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Isakara anali Netaneli,+ mwana wa Zuwara.
18 Netaneli+ mwana wa Zuwara, mtsogoleri wa fuko la Isakara, anapereka zopereka zake pa tsiku lachiwiri.