Numeri 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa ana a Zebuloni ndi Eliyabu,+ mwana wa Heloni. Numeri 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Zebuloni anali Eliyabu, mwana wa Heloni.+
7 Kumbali yake ina azimangako a fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa ana a Zebuloni ndi Eliyabu,+ mwana wa Heloni.