Numeri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mwera. Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri. Numeri 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako, a m’chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.
10 “Chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ndi asilikali awo, chizimanga msasa wawo kum’mwera. Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.
18 Kenako, a m’chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.