Numeri 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nawa mayina a amuna amene akuthandizeni: Kuchokera ku fuko la Rubeni,+ Elizuri+ mwana wa Sedeuri, Numeri 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa tsiku lachinayi panali mtsogoleri wa ana a Rubeni, Elizuri+ mwana wa Sedeuri. Numeri 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako, a m’chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.
18 Kenako, a m’chigawo cha mafuko atatu cha Rubeni+ ananyamuka m’magulu awo. Mtsogoleri wa asilikali awo anali Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.