Numeri 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri. Numeri 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Manase+ anali Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.
20 Kumbali yake imodzi azimangako a fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.