Numeri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa ana a Yosefe+ kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase,+ Gamaliyeli mwana wa Pedazuri, Numeri 7:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Pa tsiku la 8 panali mtsogoleri wa ana a Manase, Gamaliyeli+ mwana wa Pedazuri. Numeri 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mtsogoleri wa asilikali a fuko la ana a Manase+ anali Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.
10 Mwa ana a Yosefe+ kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase,+ Gamaliyeli mwana wa Pedazuri,