Genesis 41:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+
51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+