Genesis 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+ Numeri 1:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Onse olembedwa mayina a fuko la Manase analipo 32,200.+ Chivumbulutso 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mu fuko la Aseri,+ 12,000.Mu fuko la Nafitali,+ 12,000.Mu fuko la Manase,+ 12,000.
23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+