Genesis 41:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+ Ezekieli 48:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuko la Manase+ likhale ndi gawo limodzi. Gawolo liyambire kum’mawa kukafika kumadzulo ndipo lichite malire ndi gawo la fuko la Nafitali.
51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+
4 Fuko la Manase+ likhale ndi gawo limodzi. Gawolo liyambire kum’mawa kukafika kumadzulo ndipo lichite malire ndi gawo la fuko la Nafitali.