Genesis 41:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Wachiwiriyo anamutcha Efuraimu,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandipatsa ana m’dziko la masautso anga.”+ Genesis 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anapitiriza kuwadalitsa pa tsikulo.+ Anati: “Pogwiritsa ntchito dzina lako, Aisiraeli azidzadalitsana kuti,‘Mulungu akudalitse monga anadalitsira Efuraimu ndi Manase.’”+ Choncho Isiraeli anaikabe Efuraimu patsogolo pa Manase.+
52 Wachiwiriyo anamutcha Efuraimu,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandipatsa ana m’dziko la masautso anga.”+
20 Iye anapitiriza kuwadalitsa pa tsikulo.+ Anati: “Pogwiritsa ntchito dzina lako, Aisiraeli azidzadalitsana kuti,‘Mulungu akudalitse monga anadalitsira Efuraimu ndi Manase.’”+ Choncho Isiraeli anaikabe Efuraimu patsogolo pa Manase.+