Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 48:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yosefe ataona kuti bambo ake aika dzanja lawo lamanja pamutu pa Efuraimu, sizinamusangalatse.+ Choncho, anagwira dzanja la bambo ake kuti alichotse pamutu pa Efuraimu, n’kuliika pamutu pa Manase.+

  • Numeri 1:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Onse olembedwa mayina a fuko la Efuraimu+ analipo 40,500.+

  • Deuteronomo 33:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ulemerero wake ndi wofanana ndi wa mwana wa ng’ombe wamphongo woyamba kubadwa,+

      Ndipo nyanga zake ndi nyanga za ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+

      Nyanga zimenezo adzakankha nazo anthu.+

      Adzakankha nazo anthu onse pamodzi mpaka kukafika kumalekezero a dziko lapansi.

      Nyanga zimenezo ndi anthu masauzande makumimakumi a fuko la Efuraimu,+

      Ndiponso anthu masauzande a fuko la Manase.”

  • Yoswa 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yosefe anakhala mafuko awiri,+ la Manase+ ndi la Efuraimu.+ Iwowa anapatsa Alevi mizinda+ yoti azikhalamo, malo odyetserako ziweto, ndi osungirako katundu wawo, koma sanawagawire cholowa cha malo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena