-
Numeri 35:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mukayeze kunja kwa mzinda, mikono 2,000 kumbali yakum’mawa, mikono 2,000 kumbali yakum’mwera, mikono 2,000 kumbali yakumadzulo, ndi mikono 2,000 kumbali yakumpoto, kuzungulira mzinda. Amenewa akakhale malo odyetserako ziweto kwa anthu a m’mizindayo.
-