Levitiko 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Komanso, asagulitse malo odyetserako ziweto+ ozungulira mizinda yawo, chifukwa amenewo ndi malo awo mpaka kalekale. Yoswa 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ana a Isiraeli pomvera lamulo la Yehova, anapatsa Alevi+ mizindayo ndi malo ake odyetserako ziweto, kuchokera pa cholowa chawo.+ Yoswa 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anawapatsa Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.)+ Mzindawu, pamodzi ndi malo ouzungulira odyetserako ziweto, unali m’dera lamapiri la Yuda.+ 1 Mbiri 6:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Chotero ana a Isiraeli anapatsa Alevi+ mizindayo ndi malo ake odyetserako ziweto.+ 2 Mbiri 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto+ ndi madera awo+ n’kupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu,+ chifukwa Yerobowamu+ ndi ana ake anachotsa+ Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.
34 Komanso, asagulitse malo odyetserako ziweto+ ozungulira mizinda yawo, chifukwa amenewo ndi malo awo mpaka kalekale.
3 Choncho ana a Isiraeli pomvera lamulo la Yehova, anapatsa Alevi+ mizindayo ndi malo ake odyetserako ziweto, kuchokera pa cholowa chawo.+
11 Anawapatsa Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.)+ Mzindawu, pamodzi ndi malo ouzungulira odyetserako ziweto, unali m’dera lamapiri la Yuda.+
14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto+ ndi madera awo+ n’kupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu,+ chifukwa Yerobowamu+ ndi ana ake anachotsa+ Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.