Genesis 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Utembereredwe mkwiyo wawo+ chifukwa ndi wankhanza,+ ndi ukali wawo chifukwa umachita mwachiwawa.+ Ndidzawamwaza mwa Yakobo, ndipo ndidzawabalalitsa mwa Isiraeli.+ Deuteronomo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+
7 Utembereredwe mkwiyo wawo+ chifukwa ndi wankhanza,+ ndi ukali wawo chifukwa umachita mwachiwawa.+ Ndidzawamwaza mwa Yakobo, ndipo ndidzawabalalitsa mwa Isiraeli.+
8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+