Genesis 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ana awiri amene unabereka ku Iguputo kuno ine ndisanabwere, ndi ana anga.+ Efuraimu ndi Manase akhala ana anga monga alili Rubeni ndi Simiyoni.+
5 Tsopano ana awiri amene unabereka ku Iguputo kuno ine ndisanabwere, ndi ana anga.+ Efuraimu ndi Manase akhala ana anga monga alili Rubeni ndi Simiyoni.+