Numeri 35:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mizinda yonse imene mukapatse Alevi ikakwane 48. Mizindayi mukawapatse limodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+ Yoswa 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Analankhula nawo ku Silo+ m’dziko la Kanani, kuti: “Kudzera mwa Mose, Yehova analamula kuti tipatsidwe mizinda yoti tizikhalamo, pamodzi ndi malo odyetsera ziweto ozungulira mizindayo, oti tizidyetserako ziweto zathu.”+ 1 Mbiri 6:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Otsatirawa ndiwo malo amene ankakhala ana a Aroni a m’banja la Akohati,+ m’misasa yawo yokhala ndi mipanda m’madera awo,+ chifukwa maere anagwera iwowo:
7 Mizinda yonse imene mukapatse Alevi ikakwane 48. Mizindayi mukawapatse limodzi ndi malo ake odyetserako ziweto.+
2 Analankhula nawo ku Silo+ m’dziko la Kanani, kuti: “Kudzera mwa Mose, Yehova analamula kuti tipatsidwe mizinda yoti tizikhalamo, pamodzi ndi malo odyetsera ziweto ozungulira mizindayo, oti tizidyetserako ziweto zathu.”+
54 Otsatirawa ndiwo malo amene ankakhala ana a Aroni a m’banja la Akohati,+ m’misasa yawo yokhala ndi mipanda m’madera awo,+ chifukwa maere anagwera iwowo: