Yoswa 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ana a Isiraeli pomvera lamulo la Yehova, anapatsa Alevi+ mizindayo ndi malo ake odyetserako ziweto, kuchokera pa cholowa chawo.+
3 Choncho ana a Isiraeli pomvera lamulo la Yehova, anapatsa Alevi+ mizindayo ndi malo ake odyetserako ziweto, kuchokera pa cholowa chawo.+