Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 25:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Komanso, asagulitse malo odyetserako ziweto+ ozungulira mizinda yawo, chifukwa amenewo ndi malo awo mpaka kalekale.

  • Numeri 35:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Lamula ana a Isiraeli kuti pacholowa chawo cha malo, akapatseko Alevi mizinda+ yokhalamo. Akaperekenso kwa Aleviwo malo onse odyetserako ziweto ozungulira mizindayo.+

  • Numeri 35:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Malo odyetserako ziweto a mizinda imene mukapatse Aleviwo, akakhale mikono 1,000 kuchokera pampanda wa mzindawo kuzungulira mzinda wonse.

  • Yoswa 14:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yosefe anakhala mafuko awiri,+ la Manase+ ndi la Efuraimu.+ Iwowa anapatsa Alevi mizinda+ yoti azikhalamo, malo odyetserako ziweto, ndi osungirako katundu wawo, koma sanawagawire cholowa cha malo.+

  • 1 Mbiri 6:64
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 64 Chotero ana a Isiraeli anapatsa Alevi+ mizindayo ndi malo ake odyetserako ziweto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena