Numeri 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo za nsembe yachiyanjano,+ iye anapereka ng’ombe ziwiri, nkhosa zisanu zamphongo, mbuzi zisanu zamphongo, ndi ana a nkhosa asanu amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Izi n’zimene anapereka Naasoni, mwana wa Aminadabu.+
17 Ndipo za nsembe yachiyanjano,+ iye anapereka ng’ombe ziwiri, nkhosa zisanu zamphongo, mbuzi zisanu zamphongo, ndi ana a nkhosa asanu amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Izi n’zimene anapereka Naasoni, mwana wa Aminadabu.+