Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+ Levitiko 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Tsopano lamulo la nsembe yachiyanjano+ imene aliyense azipereka kwa Yehova lili motere: Malaki 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nsembe zimene Yuda ndi Yerusalemu adzapereke monga mphatso, zidzasangalatsa Yehova,+ ngati mmene zinalili kalekale kapena kuti nthawi zamakedzana.+
3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+
4 Nsembe zimene Yuda ndi Yerusalemu adzapereke monga mphatso, zidzasangalatsa Yehova,+ ngati mmene zinalili kalekale kapena kuti nthawi zamakedzana.+