-
Levitiko 16:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Munthu amene watentha zimenezi azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, akatero angathe kulowa mumsasa.
-
-
Numeri 19:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Akatha, wansembeyo achape zovala zake n’kusamba thupi lake ndi madzi. Pambuyo pake akhoza kulowa mumsasa, koma akhalebe wodetsedwa mpaka madzulo.
-