Ekisodo 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Chotero Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Lamulo la pasika ndi ili:+ Mlendo* asadye nawo.+