Levitiko 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu wamba* asadye chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala m’nyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chopatulika chilichonse. Aefeso 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+
10 “‘Munthu wamba* asadye chopatulika chilichonse.+ Mlendo wokhala m’nyumba ya wansembe kapena munthu waganyu, asadye chopatulika chilichonse.
12 Muzikumbukiranso kuti pa nthawi imene ija munali opanda Khristu,+ otalikirana+ ndi mtundu wa Isiraeli komanso alendo osadziwika pa mapangano a lonjezolo.+ Munalibe chiyembekezo+ ndipo inu munalibe Mulungu m’dzikoli.+