Ekisodo 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti apatsidwe mphamvu ndi kuyeretsedwa.+ Koma munthu wamba asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+ Mateyu 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+
33 Adye zinthu zimene aphimbira machimo kuti apatsidwe mphamvu ndi kuyeretsedwa.+ Koma munthu wamba asadye nawo, chifukwa ndi zinthu zopatulika.+
4 Kodi sanalowe m’nyumba ya Mulungu ndi kudya mitanda ya mkate woonetsa kwa Mulungu,+ umene iye ndi anthu omwe anali nawo aja sanayenera kudya malinga ndi malamulo,+ koma ansembe okha?+